Kwacha Nalelo
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2015
Lyrics
Kwacha Nalelo - Yoram Maloto
...
monga niboza kwacha nalero
kazuba kachoka kwacha nalelo
mabvuto yeve siyasala matsiku yonsa nikungoyapeza. (*2).
nati nikagona lero kapena mailo kungache na vinthu vanyowani,
kansi ayi nizinama neka mabvuto yanga nalero yanikonkha.
nimayesa masiku yonse nati kapena vinthu vingachinje, niuzeni nichifukwa cani vinthu vifunika kunkhala conco?
monga niboza kwacha nalero kazuba kachoka kwacha nalero mabvuto yeve siyasala matsiku yonsa nikungoyapeza. (*2)
matsiku yapita vinthu vamene nimafuna funa sinivipeza koma nisebeza namphamnvu. (malinga kwacha nalero).
apa napo cenje chisanga chikulu manje lero pali manyumb mbuye palibe nangu imadzi yanga, (malinga kwacha nalero).
mamotoka nikungoyaona cabe mumisewu yali fulu fulu but palibe nangu imadzi yanga, (malinga kwacha nalero).
see lyrics >>Similar Songs
More from Yoram Maloto
Listen to Yoram Maloto Kwacha Nalelo MP3 song. Kwacha Nalelo song from album Kalata is released in 2015. The duration of song is 00:04:23. The song is sung by Yoram Maloto.
Related Tags: Kwacha Nalelo, Kwacha Nalelo song, Kwacha Nalelo MP3 song, Kwacha Nalelo MP3, download Kwacha Nalelo song, Kwacha Nalelo song, Kalata Kwacha Nalelo song, Kwacha Nalelo song by Yoram Maloto, Kwacha Nalelo song download, download Kwacha Nalelo MP3 song